Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Njira yako ndi nchito zako zinakucitira izi; ici ndico coipa cako ndithu; ciri cowawa ndithu, cifikira ku mtima wako.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:18 nkhani