Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 39:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Koma ndidzakupulumutsa tsiku lomwelo, ati Yehova: ndipo sudzaperekedwa m'manja a anthu amene uwaopa.

18. Pakuti ndidzakupulumutsatu ndipo sudzagwa ndi lupanga, koma udzakhala nao moyo wako ngati cofunkha, pakuti wandikhulupirira Ine, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 39