Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 39:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pita, ukanene kwa Ebedi-Meleki Mkusi, kuti, Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Taona, ndidzafikitsira mudzi uwu mau anga kuusautsa, osaucitira zabwino; ndipo adzacitidwa pamaso pako tsiku lomwelo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 39

Onani Yeremiya 39:16 nkhani