Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 38:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga Yeremiya, namponya iye m'dzenje la Malikiya mwana wace wa mfumu, limene linali m'bwalo la kaidi; ndipo anamtsitsa Yeremiya ndi zingwe, Koma m'dzenjemo munalibe madzi, koma thope; namira Yeremiya m'thopemo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:6 nkhani