Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 38:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yeremiya anati, Sadzakuperekani. Mveranitu mau a Yehova, amene ndinena ndi inu, comweco kudzakomera inu, ndipo moyo wanu udzakhalabe.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:20 nkhani