Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 38:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yeremiya anati kwa Zedekiya, Atero Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Ngati mudzaturukira kwa akuru a mfumu ya ku Babulo, mudzakhala ndi moyo, ndipo mudziwu sudzatenthedwa ndi moto; ndipo mudzakhala ndi moyo ndi banja lanu;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:17 nkhani