Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 38:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Zedekiya anatuma, natntenga Yeremiya mneneri nalowa naye m'khomo lacitatu la nyumba ya Yehova; ndipo mfumu inati kwa Yeremiya, Ndidzakufunsa iwe kanthu; usandibisire ine kanthu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:14 nkhani