Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 37:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zedekiya mfumu analamula, ndipo anamuika Yeremiya m'bwalo la kaidi, tsiku ndi tsiku, nampatsa mkate wofuma ku mseu wa oumba mikate, mpaka unatha mkate wonse wa m'mudzi. Ndipo Yeremiya anakhala m'bwalo la kaidi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 37

Onani Yeremiya 37:21 nkhani