Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 37:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Zedekiya mwana wa Yosiya anakhala mfumu m'malo a Koniya mwana wa Yehoyakimu, amene Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo inamlowetsa mfumu m'dziko la Yuda.

2. Koma ngakhale iye, ngakhale atumiki ace, ngakhale anthu a padziko, sanamvere mau a Yehova, amene ananena mwa Yeremiya mneneri.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 37