Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali caka cacisanu ca Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mwezi wacisanu ndi cinai, anthu onse a m'Yerusalemu, ndi anthu onse ocokera m'midziya Yuda kudzaku Yerusalemu, analalikira kusala kudya pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:9 nkhani