Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Baruki anawerenga m'buku mau a Yeremiya m'nyumba ya Yehova, m'cipinda ca Gemariya mwana wa Safani mlembi, m'bwalo la kumtunda, pa khomo la cipata catsopano ca nyumba ya Yehova, m'makutu a anthu onse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:10 nkhani