Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 35:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Taonani, ndidzafikitsa pa Yuda ndi pa onse okhala m'Yerusalemu coipa conseco ndawanenera iwo; cifukwa ndanena ndi iwo, koma sanamve; ndaitana, koma iwo sanandibvomera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:17 nkhani