Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 34:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzauza, ati Yehova, ndidzabwezera iwo ku mudzi uno; ndipo adzamenyana nao, nadzaulanda, nadzautentha ndi moto; ndipo ndidzayesa midzi ya Yuda mabwinja, palibenso wokhalamo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 34

Onani Yeremiya 34:22 nkhani