Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nthawi yomweyo, ati Yehova, ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Israyeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga.

2. Atero Yehova, Anthu opulumuka m'lupanga anapeza cisomo m'cipululu; Israyeli, muja anakapuma.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31