Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova anaonekera kwa ine kale, ndi kuti, Inde, ndakukonda iwe ndi cikondi cosatha; cifukwa cace ndakukoka iwe ndi kukukomera mtima.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:3 nkhani