Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 30:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkuru wao adzakhala mwa iwo, ndi wolamulira wao adzaturuka pakati pao; ndipo ndidzamyandikitsa iye, ndipo adzayandikira kwa Ine, pakuti iye wolimba mtima kuyandikira kwa Ine ndani? ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:21 nkhani