Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 29:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzatsata iwe ndi lupanga, ndi njala, ndi caola, ndipo ndidzawapereka akhale oopsyetsa m'maufumu onse a dziko la pansi, akhale citemberero, ndi codabwitsa, ndi cotsonyetsa, ndi citonzo, kwa mitundu yonse kumene ndinawapitikitsirako;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:18 nkhani