Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aneneri amene analipo kale ndisanakhale ine, nimusanakhale inu, ananenera maiko ambiri, ndi maufumu akuru, za nkhondo, ndi za coipa, ndi za caola.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 28

Onani Yeremiya 28:8 nkhani