Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 27:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso ndinanena kwa ansembe ndi kwa anthu onsewa, kuti, Yehova atero: Musamvere mau a aneneri anu amene akunenerani inu, kuti, Taonani, zipangizo za nyumba ya Yehova zidzatengedwanso ku Babulo posacedwa; pakuti akunenerani inu zonama.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 27

Onani Yeremiya 27:16 nkhani