Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 27:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mtundu umene udzaika khosi lao pansi pa gori la mfumu ya ku Babulo, ndi kumtumikira iye, mtundu umene ndidzaulola ukhalebe m'dziko lao, ati Yehova; ndipo adzalilima, nadzakhala momwemo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 27

Onani Yeremiya 27:11 nkhani