Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 26:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi Hezekiya mfumu ya Yuda ndi Yuda wonse anamupha iye konse? kodi sanamuopa Yehova, napembedzera Yehova, ndipo Yehova analeka coipa cimene ananenera iwo? Cotero tidzaicitira miyoyo yathu coipa cacikuru.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 26

Onani Yeremiya 26:19 nkhani