Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 25:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira caka cakhumi ndi citatu ca Yosiya mwana wace wa Amoni, mfumu ya Yuda, kufikira lero lomwe, zakazi makumi awiri ndi zitatu, mau a Yehova anafika kwa ine, ndipo ndanena kwa inu, pouka mamawa ndi kunona; koma simunamvera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:3 nkhani