Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 24:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzawapatsa akhale coopsetsa coipa ku maufumu a dziko lapansi; akhale citonzo ndi nkhani ndi coseketsa, ndi citemberero, monse m'mene ndidzawapitikitsiramo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 24

Onani Yeremiya 24:9 nkhani