Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 24:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidzaika maso anga pa iwo kuti ndiwacitire iwo bwino, ndipo ndidzawabwezanso ku dziko ili: ndipo ndidzamangitsa mudzi wao, osawapasula; ndi kuwabzyala, osawazula iwo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 24

Onani Yeremiya 24:6 nkhani