Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova anandionetsa ine, ndipo, taonani, mitanga iwiri ya nkhuyu yoikidwa pakhomo pa Kacisi wa Yehova; Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo atacotsa am'nsinga Yekoniya mwana wace wa Yehoyakimu, mfumu ya Yuda, ndi akuru a Yuda, ndi amisiri ndi acipala, kuwacotsa ku Yerusalemu, nawatengera ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 24

Onani Yeremiya 24:1 nkhani