Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 23:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Za aneneri. Mtima wanga usweka m'kati mwanga, mafupa anga onse anthunthumira; ndinga munthu woledzera, ngati munthu amene vinyo anamposa; cifukwa ca Yehova, ndi cifukwa ca mau ace opatulika.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:9 nkhani