Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti dziko ladzala ndi acigololo; pakuti cifukwa ca temberero dziko lilira, mabusa a kucipululu auma; kuyenda kwao kuli koipa, ndi mphamvu yao siiri yabwino.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:10 nkhani