Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 23:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa aneneri a ku Yerusalemu ndinaona cinthu coopsetsa; acita cigololo, ayenda monama, alimbitsa manja a ocita zoipa, ndipo palibe wobwerera kuleka zoipa zace; onse akhala kwa Ine ngati Sodomu, ndi okhalamo ace ngati Gomora.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:14 nkhani