Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 22:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka iye amene amanga nyumba yace ndi cisalungamo, ndi zipinda zapamwamba ndi cosaweruza bwino; amene agwiritsa mnzace nchito osamlipira, osampatsa mphotho yace;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22

Onani Yeremiya 22:13 nkhani