Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso ndidzapereka cuma conse ca mudzi uwu, ndi zaphindu zace zonse, ndi zinthu zace zonse za mtengo wace, inde, zolemera zonse za mafumu a Yuda ndidzapereka m'manja mwa adani ao, amene adzazifunkha, nadzazitenga kunka nazo ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 20

Onani Yeremiya 20:5 nkhani