Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 2:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kaniza phazi lako lisakhale losabvala nsapato, ndi m'mero mwako musakhale ndi ludzu; koma unati, Palibe ciyembekezo, iai; pakuti ndakonda alendo, ndipo ndidzatsata pambuyo pao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2

Onani Yeremiya 2:25 nkhani