Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 18:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma, Yehova, mudziwa uphungu wao wonse wakundinenera ine kundipha ine; musakhulukire mphulupulu yao, musafafanize cimo lao pamaso panu; apunthwitsidwe pamaso panu; mucite nao m'nthawi ya mkwiyo wanu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 18

Onani Yeremiya 18:23 nkhani