Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 17:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova anatero kwa ine: Pita, nuime m'cipata ca ana a anthu, m'mene alowamo mafumu a Yuda, ndi m'mene aturukamo, ndi m'zipata zonse za Yerusalemu;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:19 nkhani