Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 17:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo akhale ndi manyazi amene andisautsa ine, koma ine ndisakhale ndi manyazi; aopsedwe iwo, koma ndisaopsedwe ine; muwatengere iwo tsiku la coipa, muwaononge ndi cionongeko cowirikiza.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:18 nkhani