Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 16:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzaitana akugwira nsomba ambiri, ati Yehova, ndipo adzawagwira iwo, pambuyo pace ndidzaitana osaka nyama ambiri, ndipo adzasaka iwo m'mapiri onse, ndi pa zitunda zonse, ndiponso m'mapanga a m'matanthwe.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16

Onani Yeremiya 16:16 nkhani