Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 16:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala, pamene udzaonetsa anthu awa mau awa onse, ndipo iwo adzati kwa iwe, Cifukwa cace nciani kuti Yehova watinenera ife coipa cacikuru ici? mphulupulu yathu ndi yanji? cimo lathu lanji limene tacimwira Yehova Mulungu wathu?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16

Onani Yeremiya 16:10 nkhani