Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkazi amene anabala asanu ndi awiri walefuka; wapereka moyo; dzuwa lace lalowa usana ulipobe; wanyazitsidwa, wathedwa nzeru; otsala ao ndidzapereka kulupanga pamaso pa adani ao, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 15

Onani Yeremiya 15:9 nkhani