Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 14:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akuru ao atuma ang'ono ao kumadzi; afika kumaenje, osapeza madzi; abwera ndi mitsuko yao yopanda kanthu; ali ndi manyazi, athedwa nzeru, apfunda mitu yao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:3 nkhani