Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 13:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Cifukwa cace ndidzabalalitsa iwo, monga ziputu zakupita, ndi mphepo ya kucipululu.

25. Ici ndi cagwera cako, gawo la muyeso wako wa kwa Ine, ati Yehova; cifukwa wandiiwala Ine, ndi kukhulupirira zonama.

26. Cifukwa cace Ine ndidzaonetsa zotopola mikawo zako, pamaso pako, ndipo manyazi ako adzaoneka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13