Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 13:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndaona zonyansa zako, ndi zigololo zako, ndi zakumemesa zako, ndi cinyerinyeri ca dama lako, pamapiri ndi m'munda. Tsoka kwa iwe, Yerusalemu! Sudzayeretsedwa; kodi zidzatero mpaka liti?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13

Onani Yeremiya 13:27 nkhani