Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 13:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo udzati kwa iwo, Atero Yehova, Taonani, ndidzadzaza ndi ciledzero onse okhala m'dziko muno, ngakhale mafumu onse amene akhala pa mpando wacifumu wa Davide, ndi ansembe, ndi aneneri, ndi onse okhala m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13

Onani Yeremiya 13:13 nkhani