Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sanamvera, sanachera khutu lao, koma onse anayenda m'kuumirira kwa mtima wao woipa; cifukwa cace ndinatengera iwo mau onse a pangano ili, limene ndinauza iwo kuti acite, koma sanacita.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11

Onani Yeremiya 11:8 nkhani