Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

limene ndinauza makolo anu tsiku lomwe ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto, m'ng'anjo ya citsulo, kuti, Mverani mau anga, ndi kuwacita, monga mwa zonse zimene ndikuuzani inu; ndipo mudzakhala anthu anga, ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wanu;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11

Onani Yeremiya 11:4 nkhani