Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti milungu yako ilingana ndi kucuruka kwa midzi yako, iwe Yuda; ndi maguwa a nsembe amene mwautsira camanyazi, alingana ndi kucuruka kwa miseu ya Yerusalemu, ndiwo maguwa akufukizirapo Baala.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11

Onani Yeremiya 11:13 nkhani