Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abwera ndi siliva wa ku Tarisi, wosulasula wopyapyala ndi golidi wa ku Ufazi, nchito ya mmisiri ndi manja a woyenga; zobvala zao ndi nsaru ya madzi ndi yofiirira; zonsezi ndi nci ito za muomba.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10

Onani Yeremiya 10:9 nkhani