Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 10:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova ndiye Mulungu woona; ndiye Mulungu wamoyo, mfumu yamuyaya; pa mkwiyo wace dziko lapansi lidzanthunthumira, ndi amitundu sangapirire ukali wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10

Onani Yeremiya 10:10 nkhani