Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 10:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

polankhula Iye, pali unyinji wa madzi m'mwamba, ndipo akweretsa nkhungu ku malekezero a dziko lapansi, alenga mphezi idzetse mvula, naturutsa mphepo m'zosungira zace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10

Onani Yeremiya 10:13 nkhani