Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kale m'Israyeli pakuombola ndi pakusinthana, kutsimikiza mlandu wonse, akatero: munthu abvula nsapato yace, naipereka kwa mnansi wace; ndiwo matsimikizidwe m'Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Rute 4

Onani Rute 4:7 nkhani