Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anthu onse anali kucipata, ndi akuru, anati, Tiri mboni ife. Yehova acite kuti mkazi wakulowayo m'nyumba mwako ange Rakele ndi Leya, amene anamanga nyumba ya Israyeli, iwo awiri; nucite iwe moyenera m'Efrata, numveke m'Betelehemu;

Werengani mutu wathunthu Rute 4

Onani Rute 4:11 nkhani