Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso Rute Mmoabu, mkazi wa Maloni ndamgula akhale mkazi wanga kuukitsa dzina la wakufayo pa colowa cace; kuti dzina la wakufayo lisaiwalike pakati pa abale ace, ndi pa cipata ca malo ace; inu ndinu mboni lero lino.

Werengani mutu wathunthu Rute 4

Onani Rute 4:10 nkhani